Mlaliki 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kuli bwino kuti usalonjeze+ kusiyana ndi kulonjeza koma osakwaniritsa zimene walonjezazo.+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:5 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),4/2022, tsa. 28 Galamukani!,4/8/1993, tsa. 16