Mlaliki 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Usalole kuti pakamwa pako pakuchimwitse,+ komanso usamanene kwa mngelo+ kuti unalakwitsa.+ Kodi Mulungu woona akwiyirenji chifukwa cha mawu ako n’kuwononga ntchito ya manja ako?+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:6 Galamukani!,4/8/1993, ptsa. 16-17
6 Usalole kuti pakamwa pako pakuchimwitse,+ komanso usamanene kwa mngelo+ kuti unalakwitsa.+ Kodi Mulungu woona akwiyirenji chifukwa cha mawu ako n’kuwononga ntchito ya manja ako?+