Mlaliki 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa chochuluka zochita pamakhala maloto,+ zinthu zachabechabe, ndi mawu ochuluka. Koma uziopa Mulungu woona yekha.+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:7 Nsanja ya Olonda,11/1/2006, tsa. 15
7 Chifukwa chochuluka zochita pamakhala maloto,+ zinthu zachabechabe, ndi mawu ochuluka. Koma uziopa Mulungu woona yekha.+