Mlaliki 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Komanso, phindu la dziko lapansi ndi la munthu aliyense,+ chifukwa ngakhale mfumu imadalira kuti munda wake ulimidwe, kuti ipindule ndi zokolola za kumundako.+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:9 Nsanja ya Olonda,11/1/2006, tsa. 14
9 Komanso, phindu la dziko lapansi ndi la munthu aliyense,+ chifukwa ngakhale mfumu imadalira kuti munda wake ulimidwe, kuti ipindule ndi zokolola za kumundako.+