Mlaliki 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Monga mmene munthu anabadwira kuchokera m’mimba mwa mayi ake, adzapitanso wamaliseche+ ngati mmene anabwerera, ndipo palibe chilichonse chimene adzatenge+ pa ntchito yake imene anaigwira mwakhama. Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:15 Nsanja ya Olonda,5/15/1998, tsa. 6
15 Monga mmene munthu anabadwira kuchokera m’mimba mwa mayi ake, adzapitanso wamaliseche+ ngati mmene anabwerera, ndipo palibe chilichonse chimene adzatenge+ pa ntchito yake imene anaigwira mwakhama.