Mlaliki 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma woipayo sizidzamuyendera bwino n’komwe,+ ndiponso sadzachulukitsa masiku ake amene ali ngati mthunzi,+ chifukwa saopa Mulungu.+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:13 Nsanja ya Olonda,2/15/1997, ptsa. 17-18
13 Koma woipayo sizidzamuyendera bwino n’komwe,+ ndiponso sadzachulukitsa masiku ake amene ali ngati mthunzi,+ chifukwa saopa Mulungu.+