Numeri 32:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma mukapanda kuchita zimenezo, ndithu mudzachimwira Yehova.+ Ndipo mukatero, dziwani kuti tchimo lanu lidzakutsatani.+ Yobu 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kuwala kwa oipa kudzazimitsidwa,+Ndipo moto wake sudzawala. Salimo 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova amasanthula anthu olungama ndi oipa omwe,+Ndipo Mulungu amadana kwambiri ndi aliyense wokonda chiwawa.+ Salimo 37:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Patsala kanthawi kochepa, woipa sadzakhalakonso.+Udzayang’ana pamene anali kukhala, ndipo sadzapezekapo.+ Yesaya 57:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Oipa alibe mtendere,”+ akutero Mulungu wanga. Mateyu 25:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndipo iwowa adzachoka kupita ku chiwonongeko chotheratu,+ koma olungama ku moyo wosatha.”+ 2 Petulo 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndipo anthu amenewa, mofanana ndi nyama zopanda nzeru zimene zimabadwira kuti zidzagwidwe ndi kuwonongedwa, amalankhula monyoza za zinthu zimene sakuzidziwa,+ moti adzawonongedwa chifukwa cha njira yawo yachiwonongeko,
23 Koma mukapanda kuchita zimenezo, ndithu mudzachimwira Yehova.+ Ndipo mukatero, dziwani kuti tchimo lanu lidzakutsatani.+
5 Yehova amasanthula anthu olungama ndi oipa omwe,+Ndipo Mulungu amadana kwambiri ndi aliyense wokonda chiwawa.+
10 Patsala kanthawi kochepa, woipa sadzakhalakonso.+Udzayang’ana pamene anali kukhala, ndipo sadzapezekapo.+
12 Ndipo anthu amenewa, mofanana ndi nyama zopanda nzeru zimene zimabadwira kuti zidzagwidwe ndi kuwonongedwa, amalankhula monyoza za zinthu zimene sakuzidziwa,+ moti adzawonongedwa chifukwa cha njira yawo yachiwonongeko,