Yesaya 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu Yehova, tikomereni mtima.+ Ife tikudalira inu.+ Tilimbitseni ndi dzanja lanu+ m’mawa uliwonse.+ Mukhale chipulumutso chathu pa nthawi ya masautso.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 33:2 Yesaya 1, ptsa. 343-346
2 Inu Yehova, tikomereni mtima.+ Ife tikudalira inu.+ Tilimbitseni ndi dzanja lanu+ m’mawa uliwonse.+ Mukhale chipulumutso chathu pa nthawi ya masautso.+