Yesaya 33:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’masiku anu, kukhulupirika kudzabweretsa chipulumutso chachikulu.+ Nazonso nzeru, kudziwa zinthu,+ ndi kuopa Yehova,+ komwe ndiko chuma chake zidzabweretsa chipulumutso chachikulu. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 33:6 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),1/2024, ptsa. 22-23
6 M’masiku anu, kukhulupirika kudzabweretsa chipulumutso chachikulu.+ Nazonso nzeru, kudziwa zinthu,+ ndi kuopa Yehova,+ komwe ndiko chuma chake zidzabweretsa chipulumutso chachikulu.