Yesaya 33:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Misewu ikuluikulu yawonongeka.+ Palibenso munthu woyenda m’njira.+ Iye waphwanya pangano+ ndipo wanyansidwa ndi mizinda.+ Sasamala za munthu aliyense.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 33:8 Yesaya 1, ptsa. 346-347
8 Misewu ikuluikulu yawonongeka.+ Palibenso munthu woyenda m’njira.+ Iye waphwanya pangano+ ndipo wanyansidwa ndi mizinda.+ Sasamala za munthu aliyense.+