Yesaya 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye ndi amene adzakhale pamalo apamwamba.+ Malo ake okhala adzakhala otetezeka m’matanthwe movuta kufikamo.+ Iye adzapatsidwa chakudya+ ndipo madzi ake sadzatha.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 33:16 Yesaya 1, ptsa. 348-349
16 Iye ndi amene adzakhale pamalo apamwamba.+ Malo ake okhala adzakhala otetezeka m’matanthwe movuta kufikamo.+ Iye adzapatsidwa chakudya+ ndipo madzi ake sadzatha.”+