Yesaya 33:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mtima wako udzalankhula motsitsa mawu+ za chinthu choopsa kuti: “Kodi mlembi ali kuti? Kodi wopereka malipiro uja ali kuti?+ Uja amawerenga nsanjayu ali kuti?”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 33:18 Yesaya 1, ptsa. 349-350
18 Mtima wako udzalankhula motsitsa mawu+ za chinthu choopsa kuti: “Kodi mlembi ali kuti? Kodi wopereka malipiro uja ali kuti?+ Uja amawerenga nsanjayu ali kuti?”+