Yesaya 33:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Palibe munthu wokhala m’dzikolo amene adzanene kuti: “Ndikudwala.”+ Anthu okhala mmenemo adzakhala amene machimo awo anakhululukidwa.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 33:24 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, article 189 Yesaya 1, ptsa. 352-355
24 Palibe munthu wokhala m’dzikolo amene adzanene kuti: “Ndikudwala.”+ Anthu okhala mmenemo adzakhala amene machimo awo anakhululukidwa.+