Yesaya 36:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma Rabisake anayankha kuti: “Kodi mbuye wanga wandituma kuti ndidzanene mawuwa kwa mbuye wanu yekha ndi kwa inuyo? Kodi sananditumenso kwa amuna amene akhala pamakomawo, kuti adye chimbudzi chawo ndi kumwa mkodzo wawo limodzi nanu?”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 36:12 Yesaya 1, tsa. 387
12 Koma Rabisake anayankha kuti: “Kodi mbuye wanga wandituma kuti ndidzanene mawuwa kwa mbuye wanu yekha ndi kwa inuyo? Kodi sananditumenso kwa amuna amene akhala pamakomawo, kuti adye chimbudzi chawo ndi kumwa mkodzo wawo limodzi nanu?”+