Yesaya 60:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “M’dziko lako simudzamvekanso zachiwawa. Mkati mwa malire ako simudzakhalanso kusakaza kapena kuwononga.+ Mipanda yako udzaitcha Chipulumutso+ ndipo zipata zako udzazitcha Chitamando. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 60:18 Nsanja ya Olonda,7/1/2002, ptsa. 17-186/15/2000, tsa. 32 Yesaya 2, tsa. 318
18 “M’dziko lako simudzamvekanso zachiwawa. Mkati mwa malire ako simudzakhalanso kusakaza kapena kuwononga.+ Mipanda yako udzaitcha Chipulumutso+ ndipo zipata zako udzazitcha Chitamando.