Yesaya 62:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma anthu amene anakolola mbewuzo ndi amene adzazidye, ndipo adzatamanda Yehova. Amene anasonkhanitsa vinyoyo ndi amene adzamumwe m’mabwalo anga oyera.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 62:9 Yesaya 2, ptsa. 344-345
9 Koma anthu amene anakolola mbewuzo ndi amene adzazidye, ndipo adzatamanda Yehova. Amene anasonkhanitsa vinyoyo ndi amene adzamumwe m’mabwalo anga oyera.”+