Yesaya 62:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma anthu amene adzakolole mbewuzo ndi amene adzazidye ndipo adzatamanda Yehova.Amene adzakolole mphesa ndi amene adzamwe vinyoyo mʼmabwalo anga oyera.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 62:9 Yesaya 2, ptsa. 344-345
9 Koma anthu amene adzakolole mbewuzo ndi amene adzazidye ndipo adzatamanda Yehova.Amene adzakolole mphesa ndi amene adzamwe vinyoyo mʼmabwalo anga oyera.”+