Yeremiya 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano konzani njira zanu ndi zochita zanu kuti zikhale zabwino+ ndipo muzimvera mawu a Yehova Mulungu wanu. Mukatero, Yehova adzasintha maganizo ake pa tsoka limene wanena kuti akugwetserani.+
13 Tsopano konzani njira zanu ndi zochita zanu kuti zikhale zabwino+ ndipo muzimvera mawu a Yehova Mulungu wanu. Mukatero, Yehova adzasintha maganizo ake pa tsoka limene wanena kuti akugwetserani.+