Yeremiya 41:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho iwo anatenga amuna onse ndi kupita kukamenyana ndi Isimaeli mwana wa Netaniya. Iwo anamupeza pafupi ndi madzi ambiri a ku Gibeoni.+
12 Choncho iwo anatenga amuna onse ndi kupita kukamenyana ndi Isimaeli mwana wa Netaniya. Iwo anamupeza pafupi ndi madzi ambiri a ku Gibeoni.+