Yeremiya 42:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ndipo mukapitiriza kunena kuti: “Ife tikupita kukakhala ku Iguputo,+ kumene sitidzaona nkhondo kapena kumva kulira kwa lipenga komanso kumene sitidzasowa chakudya, moti tikupita kukakhala kudziko limenelo,”+
14 ndipo mukapitiriza kunena kuti: “Ife tikupita kukakhala ku Iguputo,+ kumene sitidzaona nkhondo kapena kumva kulira kwa lipenga komanso kumene sitidzasowa chakudya, moti tikupita kukakhala kudziko limenelo,”+