Yeremiya 44:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine ndinali kukutumizirani atumiki anga onse aneneri, kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwatumiza.+ Ndinali kuwatuma uthenga wakuti: “Chonde, musachite zinthu zonyansa zoterezi zimene ndimadana nazo.”+
4 Ine ndinali kukutumizirani atumiki anga onse aneneri, kudzuka m’mawa kwambiri ndi kuwatumiza.+ Ndinali kuwatuma uthenga wakuti: “Chonde, musachite zinthu zonyansa zoterezi zimene ndimadana nazo.”+