Yeremiya 48:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Onse owazungulira, onse odziwa dzina lawo adzawamvera chisoni.+ Anthu inu nenani kuti, ‘Ndodo yamphamvu ndiponso yokongola yathyoka!’+
17 Onse owazungulira, onse odziwa dzina lawo adzawamvera chisoni.+ Anthu inu nenani kuti, ‘Ndodo yamphamvu ndiponso yokongola yathyoka!’+