Yeremiya 49:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Bwanji umadzitama chifukwa cha zigwa zako, zigwa zoyenda madzi,+ iwe mwana wamkazi wosakhulupirika? Iwe ukudalira chuma chako,+ ponena kuti: “Ndani angabwere kwa ine?”’”+
4 Bwanji umadzitama chifukwa cha zigwa zako, zigwa zoyenda madzi,+ iwe mwana wamkazi wosakhulupirika? Iwe ukudalira chuma chako,+ ponena kuti: “Ndani angabwere kwa ine?”’”+