Maliro 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma inu Yehova mudzakhala pampando wanu wachifumu mpaka kalekale.+ Mpando wanu wachifumuwo udzakhalapo ku mibadwomibadwo.+
19 Koma inu Yehova mudzakhala pampando wanu wachifumu mpaka kalekale.+ Mpando wanu wachifumuwo udzakhalapo ku mibadwomibadwo.+