Ezekieli 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, kodi mtengo wa mpesa+ umasiyana bwanji ndi mitengo ina yonse? Kodi kamtengo kophuka pambali pa mtengowo pakati pa mitengo ya m’nkhalango kamasiyana bwanji ndi mitengo ina?
2 “Iwe mwana wa munthu, kodi mtengo wa mpesa+ umasiyana bwanji ndi mitengo ina yonse? Kodi kamtengo kophuka pambali pa mtengowo pakati pa mitengo ya m’nkhalango kamasiyana bwanji ndi mitengo ina?