Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Mtengo wawo wa mpesa ndi wochokera ku mtengo wa mpesa wa ku Sodomu,

      Ndi kuminda ya m’mapiri a ku Gomora.+

      Zipatso zawo za mphesa ndi zakupha,

      Ndipo ndi zowawa.+

  • Salimo 80:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Munachititsa mtengo wa mpesa kuchoka mu Iguputo.+

      Munapitikitsa mitundu ya anthu kuti mubzalemo mtengowo.+

  • Yesaya 5:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndikufuna ndimuimbire nyimbo munthu amene ndimamukonda. Imeneyi ndi nyimbo yonena za munthu amene ndimamukonda, ndiponso munda wake wa mpesa.+ Wokondedwa wanga anali ndi munda wa mpesa pamalo achonde m’mbali mwa phiri.

  • Maliko 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kenako, anayamba kulankhula nawo m’mafanizo kuti: “Munthu wina analima munda wa mpesa+ ndi kumanga mpanda kuzungulira mundawo. Komanso anakumba dzenje loponderamo mphesa, ndi kumanga nsanja.+ Atatero anausiya m’manja mwa alimi+ n’kupita kudziko lina.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena