Danieli 4:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Mfumuyo ili mkati molankhula mawu amenewa, kumwamba kunamveka mawu akuti: “Tamvera iwe mfumu Nebukadinezara! ‘Ufumu wachoka m’manja mwako,+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:31 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 32
31 Mfumuyo ili mkati molankhula mawu amenewa, kumwamba kunamveka mawu akuti: “Tamvera iwe mfumu Nebukadinezara! ‘Ufumu wachoka m’manja mwako,+