Danieli 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Idzalankhula mawu otsutsana ndi Wam’mwambamwamba+ ndipo idzazunza mosalekeza oyera a Wamkulukulu.+ Idzafuna kusintha nthawi+ ndiponso lamulo+ ndipo oyerawo adzaperekedwa m’manja mwake kwa nthawi imodzi, nthawi ziwiri, ndi hafu ya nthawi.+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:25 Ulosi wa Danieli, ptsa. 141-144, 177 Nsanja ya Olonda,8/1/1994, tsa. 3111/1/1993, ptsa. 9-10
25 Idzalankhula mawu otsutsana ndi Wam’mwambamwamba+ ndipo idzazunza mosalekeza oyera a Wamkulukulu.+ Idzafuna kusintha nthawi+ ndiponso lamulo+ ndipo oyerawo adzaperekedwa m’manja mwake kwa nthawi imodzi, nthawi ziwiri, ndi hafu ya nthawi.+