Malaki 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Ine ndidzakudzudzulirani dzombe,+ ndipo silidzawononganso mbewu za m’munda mwanu. Mitengo ya mpesa ya m’munda mwanu izidzabereka zipatso nthawi zonse,”+ watero Yehova wa makamu.
11 “Ine ndidzakudzudzulirani dzombe,+ ndipo silidzawononganso mbewu za m’munda mwanu. Mitengo ya mpesa ya m’munda mwanu izidzabereka zipatso nthawi zonse,”+ watero Yehova wa makamu.