Mateyu 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mneneri Yesaya ananenera za iyeyu+ m’mawu awa: “Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti, ‘Konzani+ njira ya Yehova anthu inu! Wongolani misewu yake.’” Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:3 Nsanja ya Olonda,8/15/1997, tsa. 30
3 Mneneri Yesaya ananenera za iyeyu+ m’mawu awa: “Tamverani! Winawake akufuula m’chipululu kuti, ‘Konzani+ njira ya Yehova anthu inu! Wongolani misewu yake.’”