Mateyu 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Yesu anamuyankha kuti: “Malemba amatinso, ‘Usamuyese Yehova Mulungu wako.’”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:7 Nsanja ya Olonda,5/15/2009, tsa. 2311/15/1993, ptsa. 18-19