Mateyu 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Atapitirira pamenepo, anaona amuna enanso awiri+ apachibale, Yakobo mwana wa Zebedayo, ndi m’bale wake Yohane. Iwo anali m’ngalawa limodzi ndi bambo awo, a Zebedayo,+ akusoka maukonde awo, ndipo anawaitana.
21 Atapitirira pamenepo, anaona amuna enanso awiri+ apachibale, Yakobo mwana wa Zebedayo, ndi m’bale wake Yohane. Iwo anali m’ngalawa limodzi ndi bambo awo, a Zebedayo,+ akusoka maukonde awo, ndipo anawaitana.