Mateyu 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu onse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa,+ koma yekhayo amene adzapirire mpaka pa mapeto ndi amene adzapulumuke.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:22 Yesu—Ndi Njira, tsa. 124 Nsanja ya Olonda,8/1/1987, tsa. 28
22 Anthu onse adzadana nanu chifukwa cha dzina langa,+ koma yekhayo amene adzapirire mpaka pa mapeto ndi amene adzapulumuke.+