Mateyu 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako anaona mkuyu m’mbali mwa msewu ndipo atapita pomwepo, sanapezemo chilichonse+ koma masamba okhaokha. Choncho anauza mtengowo kuti: “Kuyambira lero sudzabalanso zipatso kwamuyaya.”+ Ndipo mkuyuwo unafota nthawi yomweyo. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:19 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 240, 244 Nsanja ya Olonda,12/15/1989, tsa. 811/15/1989, tsa. 8
19 Kenako anaona mkuyu m’mbali mwa msewu ndipo atapita pomwepo, sanapezemo chilichonse+ koma masamba okhaokha. Choncho anauza mtengowo kuti: “Kuyambira lero sudzabalanso zipatso kwamuyaya.”+ Ndipo mkuyuwo unafota nthawi yomweyo.