Mateyu 21:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kenako anapita kwa mwana wachiwiri uja n’kumuuzanso chimodzimodzi. Iye poyankha anati, ‘Ayi sindipita.’ Koma pambuyo pake anamva chisoni+ ndipo anapita. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:30 Yesu—Ndi Njira, tsa. 246 Nsanja ya Olonda,3/1/1994, ptsa. 28-291/1/1990, tsa. 8
30 Kenako anapita kwa mwana wachiwiri uja n’kumuuzanso chimodzimodzi. Iye poyankha anati, ‘Ayi sindipita.’ Koma pambuyo pake anamva chisoni+ ndipo anapita.