Mateyu 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako anauza akapolo ake kuti, ‘Phwando laukwati ndiye lakonzedwa ndithu, koma oitanidwa aja anali osayenera.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:8 Yesu—Ndi Njira, tsa. 249 Nsanja ya Olonda,1/15/1990, tsa. 9
8 Kenako anauza akapolo ake kuti, ‘Phwando laukwati ndiye lakonzedwa ndithu, koma oitanidwa aja anali osayenera.+