Mateyu 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho akapolowo anapita m’misewu ndi kusonkhanitsa onse amene anawapeza, oipa ndi abwino omwe.+ Ndipo chipinda chodyeramo phwando laukwati chinadzaza ndi anthu oyembekezera kulandira chakudya.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:10 Yesu—Ndi Njira, tsa. 249 Nsanja ya Olonda,1/15/1990, tsa. 9
10 Choncho akapolowo anapita m’misewu ndi kusonkhanitsa onse amene anawapeza, oipa ndi abwino omwe.+ Ndipo chipinda chodyeramo phwando laukwati chinadzaza ndi anthu oyembekezera kulandira chakudya.+