Mateyu 26:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Inu mukudziwa kuti pasika achitika pakangopita masiku awiri,+ ndipo Mwana wa munthu aperekedwa kuti akapachikidwe.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:2 Yesu—Ndi Njira, tsa. 266 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, tsa. 8
2 “Inu mukudziwa kuti pasika achitika pakangopita masiku awiri,+ ndipo Mwana wa munthu aperekedwa kuti akapachikidwe.”+