Mateyu 26:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Anachokanso kachiwiri+ n’kupita kukapemphera kuti: “Atate wanga, ngati sizingatheke kuti kapuyi indipitirire mpaka nditamwa ndithu, chifuniro chanu chichitike.”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:42 Nsanja ya Olonda,1/15/1988, tsa. 17
42 Anachokanso kachiwiri+ n’kupita kukapemphera kuti: “Atate wanga, ngati sizingatheke kuti kapuyi indipitirire mpaka nditamwa ndithu, chifuniro chanu chichitike.”+