Mateyu 26:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Amene anagwira Yesu aja anapita naye kwa Kayafa+ mkulu wa ansembe, kumene alembi ndi akulu anali atasonkhana.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:57 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 286-288 Nsanja ya Olonda,11/15/1990, tsa. 811/1/1990, tsa. 8
57 Amene anagwira Yesu aja anapita naye kwa Kayafa+ mkulu wa ansembe, kumene alembi ndi akulu anali atasonkhana.+