Mateyu 27:66 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 66 Choncho anapita ndi kukakhwimitsa chitetezo pamandawo mwa kutseka kwambiri mandawo ndi chimwala*+ n’kuikapo asilikali olondera. Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:66 Nsanja ya Olonda,3/1/1991, tsa. 9
66 Choncho anapita ndi kukakhwimitsa chitetezo pamandawo mwa kutseka kwambiri mandawo ndi chimwala*+ n’kuikapo asilikali olondera.