Maliko 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chotero iye anawafunsa kuti: “Kodi nanunso ndinu osazindikira ngati iwo aja?+ Kodi inunso simudziwa kuti palibe chochokera kunja kwa thupi n’kudutsa m’thupi mwa munthu chimene chingamuipitse,
18 Chotero iye anawafunsa kuti: “Kodi nanunso ndinu osazindikira ngati iwo aja?+ Kodi inunso simudziwa kuti palibe chochokera kunja kwa thupi n’kudutsa m’thupi mwa munthu chimene chingamuipitse,