Maliko 7:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma iye anatenga munthuyo ndi kuchoka naye pakhamu la anthulo kupita naye pambali. Kumeneko anapisa zala zake m’makutu a munthuyo, ndipo analavula ndi kukhudza lilime lake.+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:33 “Wotsatira Wanga,” tsa. 154 Yandikirani, ptsa. 94-95 Yesu—Ndi Njira, tsa. 138 Nsanja ya Olonda,2/15/2000, tsa. 173/1/1996, ptsa. 5-611/15/1987, tsa. 9
33 Koma iye anatenga munthuyo ndi kuchoka naye pakhamu la anthulo kupita naye pambali. Kumeneko anapisa zala zake m’makutu a munthuyo, ndipo analavula ndi kukhudza lilime lake.+
7:33 “Wotsatira Wanga,” tsa. 154 Yandikirani, ptsa. 94-95 Yesu—Ndi Njira, tsa. 138 Nsanja ya Olonda,2/15/2000, tsa. 173/1/1996, ptsa. 5-611/15/1987, tsa. 9