Maliko 8:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pakuti aliyense wochita manyazi ndi ine, komanso ndi mawu anga mu m’badwo wachigololo ndi wochimwa uno, Mwana wa munthu adzachitanso naye manyazi+ akadzafika mu ulemerero wa Atate wake limodzi ndi angelo oyera.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:38 Nsanja ya Olonda,11/1/1995, ptsa. 13-141/1/1990, tsa. 13
38 Pakuti aliyense wochita manyazi ndi ine, komanso ndi mawu anga mu m’badwo wachigololo ndi wochimwa uno, Mwana wa munthu adzachitanso naye manyazi+ akadzafika mu ulemerero wa Atate wake limodzi ndi angelo oyera.”+