Maliko 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye anatumizanso kapolo wina kwa iwo koma ameneyu anamutema m’mutu ndi kumuchitira zachipongwe.+