Maliko 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano anatsala ndi mmodzi yekha, mwana wake wokondedwa.+ Anatumizanso mwanayo kwa iwo ngati wotsirizira, n’kunena kuti, ‘Mwana wanga yekhayu akamulemekeza.’+
6 Tsopano anatsala ndi mmodzi yekha, mwana wake wokondedwa.+ Anatumizanso mwanayo kwa iwo ngati wotsirizira, n’kunena kuti, ‘Mwana wanga yekhayu akamulemekeza.’+