Maliko 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho anamugwira n’kumupha,+ ndipo anamuponya kunja kwa munda wa mpesawo.+