Maliko 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kodi tizipereka kapena tisamapereke?”+ Pozindikira chinyengo chawo, Yesu anawafunsa kuti: “Bwanji mukundiyesa? Bweretsani khobidi la dinari kuno ndilione.”+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:15 Yesu—Ndi Njira, tsa. 250 Nsanja ya Olonda,2/1/1990, tsa. 8
15 Kodi tizipereka kapena tisamapereke?”+ Pozindikira chinyengo chawo, Yesu anawafunsa kuti: “Bwanji mukundiyesa? Bweretsani khobidi la dinari kuno ndilione.”+