Maliko 12:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pamenepo Yesu, pozindikira kuti wayankha mwanzeru, anauza mlembiyo kuti: “Iwe suli kutali ndi ufumu wa Mulungu.” Ndipo panalibe amene analimba mtima kumufunsanso.+
34 Pamenepo Yesu, pozindikira kuti wayankha mwanzeru, anauza mlembiyo kuti: “Iwe suli kutali ndi ufumu wa Mulungu.” Ndipo panalibe amene analimba mtima kumufunsanso.+