Maliko 12:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Koma pamene Yesu anali kuphunzitsa m’kachisi, anayankha zonse mwa kufunsa kuti: “N’chifukwa chiyani alembi amanena kuti Khristu ndi mwana wa Davide?+ Maliko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:35 Nsanja ya Olonda,2/15/1990, tsa. 8
35 Koma pamene Yesu anali kuphunzitsa m’kachisi, anayankha zonse mwa kufunsa kuti: “N’chifukwa chiyani alembi amanena kuti Khristu ndi mwana wa Davide?+